1 Akorinto 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zinthu zonse ndi zololeka kwa ine, koma si zonse zimene zili zaphindu.+ Zinthu zonse ndi zololeka+ kwa ine, koma sindidzalola kuti chinthu china chizindilamulira.+
12 Zinthu zonse ndi zololeka kwa ine, koma si zonse zimene zili zaphindu.+ Zinthu zonse ndi zololeka+ kwa ine, koma sindidzalola kuti chinthu china chizindilamulira.+