Machitidwe 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamene anali kutumikira+ Yehova ndi kusala kudya, mzimu woyera unati: “Mwa anthu onse, mundipatulire Baranaba ndi Saulo+ kuti agwire ntchito imene ndinawaitanira.”
2 Pamene anali kutumikira+ Yehova ndi kusala kudya, mzimu woyera unati: “Mwa anthu onse, mundipatulire Baranaba ndi Saulo+ kuti agwire ntchito imene ndinawaitanira.”