Aroma 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zinthu zonse zimene zinalembedwa+ kalekale zinalembedwa kuti zitilangize.+ Malembawa amatipatsa chiyembekezo+ chifukwa amatithandiza kupirira+ ndiponso amatilimbikitsa.+ 1 Akorinto 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano zinthu zimenezi zinali kuwagwera monga zitsanzo, ndipo zinalembedwa kuti zitichenjeze+ ifeyo amene mapeto a nthawi* zino atifikira.+
4 Zinthu zonse zimene zinalembedwa+ kalekale zinalembedwa kuti zitilangize.+ Malembawa amatipatsa chiyembekezo+ chifukwa amatithandiza kupirira+ ndiponso amatilimbikitsa.+
11 Tsopano zinthu zimenezi zinali kuwagwera monga zitsanzo, ndipo zinalembedwa kuti zitichenjeze+ ifeyo amene mapeto a nthawi* zino atifikira.+