Aefeso 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 N’chifukwa chake iye akunena kuti: “Dzuka,+ wogona iwe! Uka kwa akufa,+ ndipo Khristu adzakuunika.”+ 1 Atesalonika 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero tisapitirize kugona+ ngati mmene enawo akuchitira,+ koma tikhalebe maso+ ndipo tikhalebe oganiza bwino.+
14 N’chifukwa chake iye akunena kuti: “Dzuka,+ wogona iwe! Uka kwa akufa,+ ndipo Khristu adzakuunika.”+
6 Chotero tisapitirize kugona+ ngati mmene enawo akuchitira,+ koma tikhalebe maso+ ndipo tikhalebe oganiza bwino.+