Aroma 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chitani zimenezi, makamakanso chifukwa chakuti nyengo ino mukuidziwa, kuti tili kale mu ola lakuti mudzuke ku tulo,+ pakuti chipulumutso chathu chili pafupi kwambiri tsopano kusiyana ndi nthawi imene tinakhala okhulupirira.+ 1 Akorinto 11:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiye chifukwa chake ambiri mwa inu ali ofooka ndi odwaladwala, ndipo angapo akugona+ mu imfa.
11 Chitani zimenezi, makamakanso chifukwa chakuti nyengo ino mukuidziwa, kuti tili kale mu ola lakuti mudzuke ku tulo,+ pakuti chipulumutso chathu chili pafupi kwambiri tsopano kusiyana ndi nthawi imene tinakhala okhulupirira.+