Mateyu 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndithudi, m’dzina lake mitundu ya anthu idzayembekezera zabwino.”+ Machitidwe 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiponso chipulumutso sichipezeka mwa munthu wina aliyense, pakuti palibe dzina lina+ pansi pa thambo, limene laperekedwa kwa anthu, limene tiyenera kupulumutsidwa nalo.”+
12 Ndiponso chipulumutso sichipezeka mwa munthu wina aliyense, pakuti palibe dzina lina+ pansi pa thambo, limene laperekedwa kwa anthu, limene tiyenera kupulumutsidwa nalo.”+