Machitidwe 10:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Pakuti anawamva akulankhula m’malilime ndi kulemekeza Mulungu.+ Ndiyeno Petulo anati: 1 Akorinto 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndimayamika Mulungu kuti ndimalankhula malilime ambiri kuposa nonsenu.+