Machitidwe 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno onsewo anadzazidwa ndi mzimu woyera+ ndipo anayamba kulankhula zinenero zosiyanasiyana,+ monga mmene mzimuwo unawachititsira kulankhula. Machitidwe 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Paulo atawaika manja,+ mzimu woyera unafika pa iwo, ndipo anayamba kulankhula malilime ndi kunenera.+
4 Ndiyeno onsewo anadzazidwa ndi mzimu woyera+ ndipo anayamba kulankhula zinenero zosiyanasiyana,+ monga mmene mzimuwo unawachititsira kulankhula.
6 Ndiyeno Paulo atawaika manja,+ mzimu woyera unafika pa iwo, ndipo anayamba kulankhula malilime ndi kunenera.+