Machitidwe 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno onsewo anadzazidwa ndi mzimu woyera+ ndipo anayamba kulankhula zinenero zosiyanasiyana,+ monga mmene mzimuwo unawachititsira kulankhula. Machitidwe 10:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Pakuti anawamva akulankhula m’malilime ndi kulemekeza Mulungu.+ Ndiyeno Petulo anati: 1 Akorinto 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Winanso amapatsidwa mphatso yochita ntchito zamphamvu,+ wina kunenera,+ wina kuzindikira+ mawu ouziridwa,+ wina kulankhula malilime osiyanasiyana,+ ndiponso wina kumasulira+ malilime.
4 Ndiyeno onsewo anadzazidwa ndi mzimu woyera+ ndipo anayamba kulankhula zinenero zosiyanasiyana,+ monga mmene mzimuwo unawachititsira kulankhula.
10 Winanso amapatsidwa mphatso yochita ntchito zamphamvu,+ wina kunenera,+ wina kuzindikira+ mawu ouziridwa,+ wina kulankhula malilime osiyanasiyana,+ ndiponso wina kumasulira+ malilime.