Miyambo 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Khutu lakumva ndiponso diso loona, zonsezi anazipanga ndi Yehova.+ 1 Akorinto 15:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma Mulungu amaipatsa thupi+ monga mwa kufuna kwake,+ ndipo mbewu iliyonse amaipatsa thupi lake.