Aroma 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kuoneka wolungama pamaso pa Mulungu kumeneku kungatheke mwa kukhulupirira Yesu Khristu,+ ndipo ndi kotheka kwa onse okhala ndi chikhulupiriro.+ Popeza palibe kusiyanitsa.+ Aefeso 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Palinso Ambuye mmodzi,+ chikhulupiriro chimodzi,+ ubatizo umodzi,+
22 Kuoneka wolungama pamaso pa Mulungu kumeneku kungatheke mwa kukhulupirira Yesu Khristu,+ ndipo ndi kotheka kwa onse okhala ndi chikhulupiriro.+ Popeza palibe kusiyanitsa.+