Aroma 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kuonedwa wolungama ndi Mulungu kumeneku kungatheke kwa onse amene amasonyeza kuti amakhulupirira Yesu Khristu, chifukwa palibe kusiyana.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:22 Nsanja ya Olonda,10/1/1990, tsa. 20
22 Kuonedwa wolungama ndi Mulungu kumeneku kungatheke kwa onse amene amasonyeza kuti amakhulupirira Yesu Khristu, chifukwa palibe kusiyana.+