Aroma 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kuoneka wolungama pamaso pa Mulungu kumeneku kungatheke mwa kukhulupirira Yesu Khristu,+ ndipo ndi kotheka kwa onse okhala ndi chikhulupiriro.+ Popeza palibe kusiyanitsa.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:22 Nsanja ya Olonda,10/1/1990, tsa. 20
22 Kuoneka wolungama pamaso pa Mulungu kumeneku kungatheke mwa kukhulupirira Yesu Khristu,+ ndipo ndi kotheka kwa onse okhala ndi chikhulupiriro.+ Popeza palibe kusiyanitsa.+