Aroma 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero, popeza kuti tili ndi mphatso zosiyanasiyana+ mogwirizana ndi kukoma mtima kwakukulu+ kumene tinapatsidwa, kaya tili ndi mphatso ya ulosi, tiyeni tilosere malinga ndi chikhulupiriro chimene tapatsidwa. 1 Atesalonika 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Musanyoze mawu aulosi.+
6 Chotero, popeza kuti tili ndi mphatso zosiyanasiyana+ mogwirizana ndi kukoma mtima kwakukulu+ kumene tinapatsidwa, kaya tili ndi mphatso ya ulosi, tiyeni tilosere malinga ndi chikhulupiriro chimene tapatsidwa.