Afilipi 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pakuti ndilibe wina wamtima ngati iye, amene angasamaledi+ za inu moona mtima. 1 Timoteyo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Usamanyalanyaze mphatso+ imene uli nayo, yomwe unapatsidwa mwaulosi+ ndiponso pamene bungwe la akulu linaika manja+ pa iwe.
14 Usamanyalanyaze mphatso+ imene uli nayo, yomwe unapatsidwa mwaulosi+ ndiponso pamene bungwe la akulu linaika manja+ pa iwe.