Afilipi 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chotero, mulandireni monga mwa nthawi zonse,+ mwa Ambuye ndi chimwemwe chonse. Ndipo abale okhala ngati iyeyu muziwalemekeza kwambiri,+
29 Chotero, mulandireni monga mwa nthawi zonse,+ mwa Ambuye ndi chimwemwe chonse. Ndipo abale okhala ngati iyeyu muziwalemekeza kwambiri,+