Salimo 138:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipo iwo adzaimba za njira za Yehova,+Pakuti ulemerero wa Yehova ndi waukulu.+ Yesaya 40:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ulemerero wa Yehova ndithu udzaonekera+ ndipo anthu onse adzauonera limodzi,+ pakuti pakamwa pa Yehova m’pamene panena zimenezi.”+ Yesaya 60:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 “Imirira+ mkazi iwe! Onetsa kuwala kwako,+ pakuti kuwala kwako kwafika,+ ndipo ulemerero wa Yehova wakuunika.+
5 Ulemerero wa Yehova ndithu udzaonekera+ ndipo anthu onse adzauonera limodzi,+ pakuti pakamwa pa Yehova m’pamene panena zimenezi.”+
60 “Imirira+ mkazi iwe! Onetsa kuwala kwako,+ pakuti kuwala kwako kwafika,+ ndipo ulemerero wa Yehova wakuunika.+