2 Akorinto 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipotu, pamene tinafika ku Makedoniya,+ thupi lathu silinapumule,+ koma masautso amitundumitundu anapitirizabe kutigwera.+ Kunja anali kulimbana nafe, mkati tinali kukhala mwamantha.
5 Ndipotu, pamene tinafika ku Makedoniya,+ thupi lathu silinapumule,+ koma masautso amitundumitundu anapitirizabe kutigwera.+ Kunja anali kulimbana nafe, mkati tinali kukhala mwamantha.