Machitidwe 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chipolowe chija chitatha, Paulo anaitanitsa ophunzira. Atawalimbikitsa ndi kutsanzikana nawo,+ ananyamuka ulendo wopita ku Makedoniya.+
20 Chipolowe chija chitatha, Paulo anaitanitsa ophunzira. Atawalimbikitsa ndi kutsanzikana nawo,+ ananyamuka ulendo wopita ku Makedoniya.+