1 Akorinto 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndidzafika kwa inu pochokera ku Makedoniya, pakuti ndipita ku Makedoniya.+ 1 Timoteyo 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Paja nditatsala pang’ono kupita ku Makedoniya, ndinakulimbikitsa kuti ukhalebe ku Efeso.+ Ndikukulimbikitsanso kuti ukhalebe komweko, uletse+ anthu ena ake kuti asaphunzitse chiphunzitso chosiyana ndi chathu,+
3 Paja nditatsala pang’ono kupita ku Makedoniya, ndinakulimbikitsa kuti ukhalebe ku Efeso.+ Ndikukulimbikitsanso kuti ukhalebe komweko, uletse+ anthu ena ake kuti asaphunzitse chiphunzitso chosiyana ndi chathu,+