Agalatiya 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndine wodabwa kuti mwapatutsidwa mwamsanga, kuchoka kwa Iye+ amene anakuitanani mwa kukoma mtima kwakukulu kwa Khristu,+ ndipo mwakopeka ndi uthenga wabwino wamtundu wina.+ 2 Yohane 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aliyense amene amachita zosemphana ndi zimene Khristu amaphunzitsa,+ ndiye kuti akukana Mulungu.+ Koma amene amachita zinthu mogwirizana ndi zimene iye amaphunzitsa, amavomerezedwa ndi Atate ndiponso Mwana.+
6 Ndine wodabwa kuti mwapatutsidwa mwamsanga, kuchoka kwa Iye+ amene anakuitanani mwa kukoma mtima kwakukulu kwa Khristu,+ ndipo mwakopeka ndi uthenga wabwino wamtundu wina.+
9 Aliyense amene amachita zosemphana ndi zimene Khristu amaphunzitsa,+ ndiye kuti akukana Mulungu.+ Koma amene amachita zinthu mogwirizana ndi zimene iye amaphunzitsa, amavomerezedwa ndi Atate ndiponso Mwana.+