Aheberi 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti kwenikweni timachita nawo zimene Khristu akuchita,+ ngati zinthu zimene tinali kudalira pa chiyambi, tazigwira mwamphamvu mpaka mapeto.+ 1 Yohane 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Aliyense amene amakana Mwana sangakhale pa ubwenzi ndi Atate.+ Amene wavomereza+ Mwana amakhalanso pa ubwenzi ndi Atate.+
14 Pakuti kwenikweni timachita nawo zimene Khristu akuchita,+ ngati zinthu zimene tinali kudalira pa chiyambi, tazigwira mwamphamvu mpaka mapeto.+
23 Aliyense amene amakana Mwana sangakhale pa ubwenzi ndi Atate.+ Amene wavomereza+ Mwana amakhalanso pa ubwenzi ndi Atate.+