Yohane 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu mukanandidziwa ine, mukanadziwanso Atate wanga. Kuyambira panopa mwawadziwa ndipo mwawaona.”+ 1 Yohane 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Aliyense amene amavomereza kuti Yesu Khristu ndi Mwana wa Mulungu,+ amakhala wogwirizana ndi Mulungu ndipo Mulungu amakhala wogwirizana naye.+
15 Aliyense amene amavomereza kuti Yesu Khristu ndi Mwana wa Mulungu,+ amakhala wogwirizana ndi Mulungu ndipo Mulungu amakhala wogwirizana naye.+