Yohane 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yesu anamuuza kuti: “Ine ndine njira,+ choonadi+ ndi moyo.+ Palibe amene amafika kwa Atate osadzera mwa ine.+ 3 Yohane 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndinalemba nkhani inayake kumpingo, koma Diotirefe, amene amakonda kukhala woyamba+ pakati pawo, salandira mwaulemu+ chilichonse chochokera kwa ife.+
6 Yesu anamuuza kuti: “Ine ndine njira,+ choonadi+ ndi moyo.+ Palibe amene amafika kwa Atate osadzera mwa ine.+
9 Ndinalemba nkhani inayake kumpingo, koma Diotirefe, amene amakonda kukhala woyamba+ pakati pawo, salandira mwaulemu+ chilichonse chochokera kwa ife.+