Mateyu 20:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Amene akufuna kukhala woyamba pakati panu ayenera kukhala kapolo wanu.+ Machitidwe 20:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndipo pakati panu anthu ena adzayamba kulankhula zinthu zopotoka+ kuti apatutse ophunzira aziwatsatira.+ Afilipi 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musachite chilichonse ndi mtima wokonda mikangano+ kapena wodzikuza,+ koma modzichepetsa, ndi kuona ena kukhala okuposani.+
30 Ndipo pakati panu anthu ena adzayamba kulankhula zinthu zopotoka+ kuti apatutse ophunzira aziwatsatira.+
3 Musachite chilichonse ndi mtima wokonda mikangano+ kapena wodzikuza,+ koma modzichepetsa, ndi kuona ena kukhala okuposani.+