21 Tsopano izi zitatha, Paulo anatsimikiza mumtima mwake kupita ku Yerusalemu,+ kudzera ku Makedoniya+ ndi ku Akaya. Iye anati: “Ndikakafika kumeneko, ndiyeneranso kukaona ku Roma.”+
16 Kuti ndikadzacheza nanu pang’ono ndidzapite ku Makedoniya,+ ndipo ndikadzachoka ku Makedoniya ndidzabwerenso kwa inu+ kuti mudzandiperekeze+ popita ku Yudeya.