2 Akorinto 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kwa amene akupita kukawonongedwawo ndife fungo lochokera ku imfa kupita ku imfa,+ koma kwa amene akupita kukapulumukawo ndife fungo lochokera ku moyo kupita ku moyo. Ndipo ndani ali woyenerera kugwira ntchito imeneyi?+
16 Kwa amene akupita kukawonongedwawo ndife fungo lochokera ku imfa kupita ku imfa,+ koma kwa amene akupita kukapulumukawo ndife fungo lochokera ku moyo kupita ku moyo. Ndipo ndani ali woyenerera kugwira ntchito imeneyi?+