Afilipi 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pa zinthu zonse, ndimapeza mphamvu kuchokera kwa iye amene amandipatsa mphamvu.+ Chivumbulutso 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ‘Ndikudziwa masautso ako ndi umphawi wako, koma ndiwe wolemera.+ Ndikudziwanso za kutonza kwa odzitcha Ayudawo,+ pamene si Ayuda, koma ndiwo sunagoge wa Satana.+
9 ‘Ndikudziwa masautso ako ndi umphawi wako, koma ndiwe wolemera.+ Ndikudziwanso za kutonza kwa odzitcha Ayudawo,+ pamene si Ayuda, koma ndiwo sunagoge wa Satana.+