1 Akorinto 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nthawi zonse ndimayamika Mulungu chifukwa cha inu, poona kukoma mtima kwakukulu+ kwa Mulungu kumene anakusonyezani kudzera mwa Khristu Yesu,+ 2 Akorinto 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inuyo mwavomereza kale, ngakhale kuti m’pang’ono pokha, kuti ifeyo ndife chifukwa choti mudzitamandire,+ ngati mmene inuyonso mudzakhalire chifukwa choti ifeyo tidzadzitamandire m’tsiku la Ambuye wathu Yesu.+
4 Nthawi zonse ndimayamika Mulungu chifukwa cha inu, poona kukoma mtima kwakukulu+ kwa Mulungu kumene anakusonyezani kudzera mwa Khristu Yesu,+
14 Inuyo mwavomereza kale, ngakhale kuti m’pang’ono pokha, kuti ifeyo ndife chifukwa choti mudzitamandire,+ ngati mmene inuyonso mudzakhalire chifukwa choti ifeyo tidzadzitamandire m’tsiku la Ambuye wathu Yesu.+