1 Akorinto 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 mupereke munthu ameneyu kwa Satana+ kuti thupilo liwonongedwe, n’cholinga choti mzimuwo+ upulumutsidwe m’tsiku la Ambuye.+ 1 Akorinto 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 ndipo Mulungu amaweruza amene ali kunja?+ “M’chotseni pakati panu munthu woipayo.”+
5 mupereke munthu ameneyu kwa Satana+ kuti thupilo liwonongedwe, n’cholinga choti mzimuwo+ upulumutsidwe m’tsiku la Ambuye.+