1 Akorinto 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho ndinafika kwa inu ndili wofooka, ndipo ndinali kunjenjemera+ ndi mantha. 2 Akorinto 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano ineyo Paulo, ndikukudandaulirani mwa kufatsa+ ndi kukoma mtima+ kwa Khristu, ngakhale kuti ndimaoneka wosanunkha kanthu+ ndikakhala pakati panu, koma wolimba mtima polankhula nanu ndili kwina.+
10 Tsopano ineyo Paulo, ndikukudandaulirani mwa kufatsa+ ndi kukoma mtima+ kwa Khristu, ngakhale kuti ndimaoneka wosanunkha kanthu+ ndikakhala pakati panu, koma wolimba mtima polankhula nanu ndili kwina.+