Machitidwe 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo popeza kuti ntchito yawo inali imodzi, anakhala kunyumba kwawoko. Iwo ankagwira ntchito pamodzi,+ pakuti onse anali amisiri opanga mahema. 1 Akorinto 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho mphoto yanga ndi chiyani? Ndi yakuti polengeza uthenga wabwino ndipereke uthengawo kwaulere,+ kuti ndisagwiritse ntchito molakwa ufulu wanga pa zinthu zokhudzana ndi uthenga wabwino.
3 Ndipo popeza kuti ntchito yawo inali imodzi, anakhala kunyumba kwawoko. Iwo ankagwira ntchito pamodzi,+ pakuti onse anali amisiri opanga mahema.
18 Choncho mphoto yanga ndi chiyani? Ndi yakuti polengeza uthenga wabwino ndipereke uthengawo kwaulere,+ kuti ndisagwiritse ntchito molakwa ufulu wanga pa zinthu zokhudzana ndi uthenga wabwino.