Machitidwe 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pamenepo khamu la anthu linanyamuka pamodzi ndi kuukira atumwiwo. Ndipo akuluakulu a boma aja, anavula atumwiwo malaya awo akunja mochita kuwang’ambira ndi kulamula kuti awakwapule ndi zikoti.+
22 Pamenepo khamu la anthu linanyamuka pamodzi ndi kuukira atumwiwo. Ndipo akuluakulu a boma aja, anavula atumwiwo malaya awo akunja mochita kuwang’ambira ndi kulamula kuti awakwapule ndi zikoti.+