Machitidwe 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako gulu lonselo linanyamuka nʼkuukira atumwiwo. Ndipo akuluakulu a zamalamulowo, anavula atumwiwo malaya awo mochita kuwangʼambira nʼkulamula kuti awakwapule ndi ndodo.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:22 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 129 Nsanja ya Olonda,2/15/1999, tsa. 27
22 Kenako gulu lonselo linanyamuka nʼkuukira atumwiwo. Ndipo akuluakulu a zamalamulowo, anavula atumwiwo malaya awo mochita kuwangʼambira nʼkulamula kuti awakwapule ndi ndodo.+