Machitidwe 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pamenepo khamu la anthu linanyamuka pamodzi ndi kuukira atumwiwo. Ndipo akuluakulu a boma aja, anavula atumwiwo malaya awo akunja mochita kuwang’ambira ndi kulamula kuti awakwapule ndi zikoti.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:22 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 129 Nsanja ya Olonda,2/15/1999, tsa. 27
22 Pamenepo khamu la anthu linanyamuka pamodzi ndi kuukira atumwiwo. Ndipo akuluakulu a boma aja, anavula atumwiwo malaya awo akunja mochita kuwang’ambira ndi kulamula kuti awakwapule ndi zikoti.+