1 Akorinto 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa ngati mupereka chitamando ndi mphatso ya mzimu, kodi munthu wamba anganene bwanji “Ame”+ pa kuyamika kwanu, posadziwa zimene mukunena? Chivumbulutso 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Kwa mngelo wa mpingo wa ku Laodikaya,+ lemba kuti: Izi ndi zimene akunena Ame,+ mboni+ yokhulupirika+ ndi yoona,+ woyamba wa chilengedwe cha Mulungu.+
16 Chifukwa ngati mupereka chitamando ndi mphatso ya mzimu, kodi munthu wamba anganene bwanji “Ame”+ pa kuyamika kwanu, posadziwa zimene mukunena?
14 “Kwa mngelo wa mpingo wa ku Laodikaya,+ lemba kuti: Izi ndi zimene akunena Ame,+ mboni+ yokhulupirika+ ndi yoona,+ woyamba wa chilengedwe cha Mulungu.+