1 Akorinto 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Takhala opusa+ chifukwa cha Khristu, koma inu mwakhala ochenjera+ mwa Khristu. Ife ndife ofooka,+ inu ndinu amphamvu.+ Inu muli ndi mbiri yabwino,+ koma ifeyo tikunyozedwa.+
10 Takhala opusa+ chifukwa cha Khristu, koma inu mwakhala ochenjera+ mwa Khristu. Ife ndife ofooka,+ inu ndinu amphamvu.+ Inu muli ndi mbiri yabwino,+ koma ifeyo tikunyozedwa.+