1 Akorinto 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Takhala opusa+ chifukwa cha Khristu, koma inu mwakhala ochenjera mwa Khristu. Ife ndife ofooka, inu ndinu amphamvu. Inu mukulemekezedwa, koma ifeyo tikunyozedwa. 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:10 Nsanja ya Olonda,5/15/1988, tsa. 27
10 Takhala opusa+ chifukwa cha Khristu, koma inu mwakhala ochenjera mwa Khristu. Ife ndife ofooka, inu ndinu amphamvu. Inu mukulemekezedwa, koma ifeyo tikunyozedwa.