Aroma 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pokonda abale,+ khalani ndi chikondi chenicheni pakati panu. Posonyezana ulemu,+ khalani patsogolo. Akolose 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Timatero chifukwa tinamva za chikhulupiriro chanu mwa Khristu Yesu, ndi chikondi chanu pa oyera onse,+
10 Pokonda abale,+ khalani ndi chikondi chenicheni pakati panu. Posonyezana ulemu,+ khalani patsogolo.
4 Timatero chifukwa tinamva za chikhulupiriro chanu mwa Khristu Yesu, ndi chikondi chanu pa oyera onse,+