Aroma 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma tsopano ndatsala pang’ono kupita ku Yerusalemu kukatumikira oyera.+ Filimoni 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 pamene ndikumva za chikondi ndi chikhulupiriro chimene uli nacho kwa Ambuye Yesu ndi kwa oyera onse.+ Aheberi 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti Mulungu si wosalungama woti angaiwale ntchito yanu ndi chikondi chimene munachisonyeza pa dzina lake,+ mwa kutumikira oyera+ ndipo mukupitiriza kuwatumikira.
5 pamene ndikumva za chikondi ndi chikhulupiriro chimene uli nacho kwa Ambuye Yesu ndi kwa oyera onse.+
10 Pakuti Mulungu si wosalungama woti angaiwale ntchito yanu ndi chikondi chimene munachisonyeza pa dzina lake,+ mwa kutumikira oyera+ ndipo mukupitiriza kuwatumikira.