Aroma 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 monga mmene Malemba amanenera kuti: “Palibe munthu wolungama ndi mmodzi yemwe.+ Agalatiya 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Sindikukankhira kumbali kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu,+ chifukwa ngati munthu amakhala wolungama kudzera mwa chilamulo,+ ndiye kuti Khristu anangofa pachabe.+
21 Sindikukankhira kumbali kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu,+ chifukwa ngati munthu amakhala wolungama kudzera mwa chilamulo,+ ndiye kuti Khristu anangofa pachabe.+