Aroma 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wina amaona tsiku lina ngati loposa linzake,+ koma wina amaona tsiku lina mofanana ndi masiku ena onse.+ Choncho munthu aliyense akhale wotsimikiza ndi mtima wonse m’maganizo mwake.
5 Wina amaona tsiku lina ngati loposa linzake,+ koma wina amaona tsiku lina mofanana ndi masiku ena onse.+ Choncho munthu aliyense akhale wotsimikiza ndi mtima wonse m’maganizo mwake.