Mateyu 10:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Amene wakulandirani walandiranso ine, ndipo amene walandira ine walandiranso amene anandituma.+ Yohane 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndithudi ndikukuuzani, Wolandira aliyense amene ine ndamutuma walandiranso ine.+ Ndipo amene walandira ine, walandiranso amene anandituma.”+
20 Ndithudi ndikukuuzani, Wolandira aliyense amene ine ndamutuma walandiranso ine.+ Ndipo amene walandira ine, walandiranso amene anandituma.”+