15 Pakuti ngakhale mutakhala ndi aphunzitsi+ 10,000 mwa Khristu, ndithudi mulibe abambo ambiri,+ pakuti mwa Khristu Yesu ndakhala bambo anu kudzera mwa uthenga wabwino.+
11 Mogwirizana ndi zimenezi, inu mukudziwa bwino mmene tinali kudandaulira kwa aliyense wa inu, monga mmene bambo+ amachitira ndi ana ake, kukulimbikitsani+ ndi kukuchondererani,