Genesis 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho Sarai anauza Abulamu kuti: “Yehova ananditseka kuti ndisabereke ana.+ Tsopano gonani ndi kapolo wanga. Mwinatu ndingapeze ana kuchokera kwa iye.”+ Chotero Abulamu anamvera mawu a Sarai.+ Aroma 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Izi zikutanthauza kuti, si ana akuthupi+ amene alidi ana a Mulungu,+ koma ana a lonjezo+ ndiwo amayesedwa mbewu.
2 Choncho Sarai anauza Abulamu kuti: “Yehova ananditseka kuti ndisabereke ana.+ Tsopano gonani ndi kapolo wanga. Mwinatu ndingapeze ana kuchokera kwa iye.”+ Chotero Abulamu anamvera mawu a Sarai.+
8 Izi zikutanthauza kuti, si ana akuthupi+ amene alidi ana a Mulungu,+ koma ana a lonjezo+ ndiwo amayesedwa mbewu.