Yesaya 57:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi mukusangalala chifukwa cha kuvutika kwa ndani?+ Kodi mukuyasamulira ndani pakamwa panu, ndi kum’tulutsira lilime?+ Kodi inu si inu ana a machimo, mbewu ya chinyengo,+ Agalatiya 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma mwana amene anabadwa kwa mdzakazi uja anabadwa monga mmene ana onse amabadwira,+ pamene mwana winayo amene anabadwa kwa mkazi amene anali mfulu anabadwa mwa lonjezo.+
4 Kodi mukusangalala chifukwa cha kuvutika kwa ndani?+ Kodi mukuyasamulira ndani pakamwa panu, ndi kum’tulutsira lilime?+ Kodi inu si inu ana a machimo, mbewu ya chinyengo,+
23 Koma mwana amene anabadwa kwa mdzakazi uja anabadwa monga mmene ana onse amabadwira,+ pamene mwana winayo amene anabadwa kwa mkazi amene anali mfulu anabadwa mwa lonjezo.+