Aroma 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pajatu mdulidwe+ ndi waphindu pokhapokha ngati iweyo umatsatiradi chilamulo.+ Koma ngati umaphwanya chilamulo, ndiye kuti mdulidwe+ wako ndi wopanda tanthauzo.+ Agalatiya 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti onse odalira ntchito za chilamulo ndi otembereredwa, chifukwa Malemba amati: “Ndi wotembereredwa aliyense wosapitiriza kuyenda m’zinthu zonse zolembedwa mumpukutu wa Chilamulo ndi kuzichita.”+
25 Pajatu mdulidwe+ ndi waphindu pokhapokha ngati iweyo umatsatiradi chilamulo.+ Koma ngati umaphwanya chilamulo, ndiye kuti mdulidwe+ wako ndi wopanda tanthauzo.+
10 Pakuti onse odalira ntchito za chilamulo ndi otembereredwa, chifukwa Malemba amati: “Ndi wotembereredwa aliyense wosapitiriza kuyenda m’zinthu zonse zolembedwa mumpukutu wa Chilamulo ndi kuzichita.”+