Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 8:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Tsopano Saulo anayamba kuzunza mpingo mwankhanza. Anali kulowa m’nyumba ndi nyumba, ndi kukokera panja amuna ndi akazi omwe, n’kukawaponya m’ndende.+

  • Machitidwe 9:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma Saulo anapitiriza kuopseza ophunzira+ a Ambuye komanso anali wofunitsitsa kuwapha.+ Choncho anapita kwa mkulu wa ansembe

  • Machitidwe 22:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndinazunza otsatira Njira imeneyi mpaka imfa.+ Ndinali kumanga amuna ndi akazi ndi kuwapereka kundende.+

  • Machitidwe 26:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Nthawi zambiri ndinawapatsa chilango m’masunagoge onse,+ poyesa kuwakakamiza kuti akane chikhulupiriro chawo. Popeza ndinali nditakwiya nawo kwambiri, ndinafika pa kuwazunza ngakhale m’mizinda yakunja.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena