Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 9:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma Saulo anapitiriza kuopseza ophunzira+ a Ambuye komanso anali wofunitsitsa kuwapha.+ Choncho anapita kwa mkulu wa ansembe

  • Machitidwe 22:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndinazunza otsatira Njira imeneyi mpaka imfa.+ Ndinali kumanga amuna ndi akazi ndi kuwapereka kundende.+

  • Machitidwe 26:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndipo zimenezi ndinazichitadi mu Yerusalemu. Oyera ambiri ndinawatsekera m’ndende,+ nditapatsidwa mphamvu ndi ansembe aakulu.+ Pamene anafuna kuwapha, ine ndinali kuvomereza.

  • 1 Akorinto 15:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ineyo ndine wamng’ono kwambiri+ mwa atumwi onse, ndipo si ine woyenera kutchedwa mtumwi, chifukwa ndinazunza+ mpingo wa Mulungu.

  • Agalatiya 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Munamva ndithu zimene ndinali kuchita ndili m’Chiyuda,+ kuti ndinkazunza kwambiri+ mpingo wa Mulungu ndi kupitirizabe kuuwononga.+

  • Afilipi 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kunena za kudzipereka, ndinali kuzunza mpingo.+ Kunena za chilungamo mwa kutsatira chilamulo, ndinakhaladi wopanda chifukwa chondinenezera.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena