Machitidwe 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano Saulo anayamba kuzunza mpingo mwankhanza. Anali kulowa m’nyumba ndi nyumba, ndi kukokera panja amuna ndi akazi omwe, n’kukawaponya m’ndende.+ Machitidwe 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma Saulo anapitiriza kuopseza ophunzira+ a Ambuye komanso anali wofunitsitsa kuwapha.+ Choncho anapita kwa mkulu wa ansembe Agalatiya 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munamva ndithu zimene ndinali kuchita ndili m’Chiyuda,+ kuti ndinkazunza kwambiri+ mpingo wa Mulungu ndi kupitirizabe kuuwononga.+
3 Tsopano Saulo anayamba kuzunza mpingo mwankhanza. Anali kulowa m’nyumba ndi nyumba, ndi kukokera panja amuna ndi akazi omwe, n’kukawaponya m’ndende.+
9 Koma Saulo anapitiriza kuopseza ophunzira+ a Ambuye komanso anali wofunitsitsa kuwapha.+ Choncho anapita kwa mkulu wa ansembe
13 Munamva ndithu zimene ndinali kuchita ndili m’Chiyuda,+ kuti ndinkazunza kwambiri+ mpingo wa Mulungu ndi kupitirizabe kuuwononga.+